ZEZE Ringtones
17 ringtones matching "ZEZE". Here you can browse, listen and download ZEZE Ringtones for free. Best ZEZE Ringtones Download with MP3 file format for your Android mobile phone.
30
@Merjem
0
30
@Annabella
185,189
30
@Gayane
1,308
5
@Iestyn
136
30
@Ayana
255
30
@Aiym
260
20
@Medina
1479
30
@Thomas
4,397
30
@Aruzhan
423
30
@Inkar
171
30
@Sona
187
Kale likati lizibwelela, kale likati lizibwelela
Kale likati lizibwelela, kale likati lizibwelela
Ndikakumbukila komwe ndikuchokela
Ndikakumbukila komwe ndikuchokela eish
Ndati ndikakumbukila komwe ndikuchokela
Ndikakumbukila komwe ndikuchokela
Ndati kale, ndikupanga zawana
Chalila, magalimoto a dongo
Ndati kale, ndikupanga zawana
Chalila, magalimoto a dongo
Eish ndati kale kale kale kale
Kale kale kale kale
Kale kale kale kale
Kale kale kale kale
Kale langa likati libwelenso ayi ayi ayi ayi ayi ayi
Tinkakhala opanda nkhawa ayi ayi ayi ayi ayi ayi
Tinkati Bhali nkede bhali nkede
Bhali nkede bhali nkede
Bhali nkede bhali nkede
Bhali nkede bhali nkede
Bhali nkede bhali nkede
Bhali nkede bhali nkede
Bhali nkede bhali nkede
Bhali nkede
Kale likati lizibwelela, kale likati lizibwelela
Kale likati lizibwelela, kale likati lizibwelela
Ndikakumbukila komwe ndikuchokela
Ndikakumbukila komwe ndikuchokela eish
Ndati ndikakumbukila komwe ndikuchokela
Ndikakumbukila komwe ndikuchokela
Kale langa likati libwelenso ayi ayi ayi ayi ayi ayi
Tinkakhala opanda nkhawa ayi ayi ayi ayi ayi ayi
Tinkati Bhali nkede bhali nkede
Bhali nkede bhali nkede
Bhali nkede bhali nkede
Bhali nkede bhali nkede
Bhali nkede bhali nkede
Bhali nkede bhali nkede
Bhali nkede bhali nkede
Bhali nkede
30
@Sebastian
7,450
28
@Mathieu
119
15
@Liam
178
Mmmh hmm hmm hmm
Set up, set up
(Eyo tiyeni)
(Tiyeni tiyeni tiyeni)
(Eish sha sha)
Wakutuma ndani
Ungandiuze chani
Wakutuma ndani
Ungandiuze chani
Munthu wopanda plan
Wochulukitsa nkhani
Ungandiuze chani
Ungandiuze chani
Wakutuma ndani
Ungandiuze chani
Wakutuma ndani
Ungandiuze chani
Munthu wopanda plan
Wochulukitsa nkhani
Ungandiuze chani
Ungandiuze chani
Chule chule
Iwe bwantasa wakutuma ndani
Bwantasa kuti ubekeshule
Bwantasa mwana wachipongwe
Chule chule
Iwe bwantasa wakutuma ndani
Bwantasa kuti ubekeshule, (uuh)
Bwantasa mwana wachipongwe
Ndakula movutika
Man dekhani
Mukachulukitsa nkhani
Ife tingoku wekani
Ndakula movutika
Man dekhani
Mukachulukitsa nkhani
Ife tingoku wekani
Wachibanda ndani
Zakulembani
Akufuna plan ndani, usachulutse nkhani
Uli ndizinga?
Uka blaka tisenza
Ibweleso ina round
Mpakana titentha
Koma iwe iwe
Iweso nde ndani
Kodi wasonkha?
Kutizembelera pompa
Usamayese iwe iwe iwe
Iweso nde ndani? (wakutuma ndani)
Kodi wasonkha?
Kutizembelera pompa
Usamayese iwe
Ndakula movutika
Man dekhani
Mukachulukitsa nkhani
Ife tingoku wekani
Ndakula movutika
Man dekhani
Mukachulukitsa nkhani
Ife tingoku wekani
Chule chule
Iwe bwantasa wakutuma ndani
Bwantasa kuti ubekeshule
Bwantasa mwana wachipongwe
Chule chule
Iwe bwantasa wakutuma ndani
Bwantasa kuti ubekeshule
Bwantasa mwana wachipongwe
Aaah uh
Aaah uh
15
@Felix
629
30
@Emile
179
Eyo VJ, eish!
Tiyeni, tiyeni
Tiyeni, tiyeni, tiyeni eish!
Pita, ukanene ndathela pano
Anthu onsewa adziwe, ndathela pano
Ndati pita, ukanene ndathela pano
Anthu onsewa adziwe, ndathela pano
Ndiye undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Ndati undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Akabwela kudzafunsa, usamangike iwe
Awuze adziwe, uli ndi ine
Akabwela kudzafunsa, usamangike iwe
Awuze adziwe, uli ndi ine
Poti ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndati ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndati ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndiye Pita ukanene, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndati pita ukanene, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndati ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano eish
Ndati ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Ndati undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Akabwela kudzafunsa, usamangike iwe
Awuze adziwe, uli ndi ine
Akabwela kudzafunsa, usamangike iwe
Awuze adziwe, uli ndi ine
Ndiye pita ukanene, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndati pita ukanene, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndati ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano eish
Ndati ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
30
@Emine
120